Yohane 15:4 BL92

4 Khalani mwa Ine, ndi Ine mwa inu. Monga nthambi siingathe kubala cipatso pa yokha, ngati siikhala mwampesa; motere mulibe inunso ngati simukhala mwa Ine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 15

Onani Yohane 15:4 nkhani