2 Adzakuturutsani m'masunagoge; koma ikudza nthawi imene yense wakupha inu adzayesa kuti atumikira Mulungu,
Werengani mutu wathunthu Yohane 16
Onani Yohane 16:2 nkhani