Yohane 16:20 BL92

20 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, kuti mudzalira ndi kubuma maliro inu, koma dziko lapansi lidzakondwera; mudzacita cisoni inu, koma cisoni canu cidzasandulika cimwemwe.

Werengani mutu wathunthu Yohane 16

Onani Yohane 16:20 nkhani