30 Tsopano tidziwa kuti mudziwa zonse, ndipo mulibe kusowa kuti wina akafunse Inu; mwa ici tikhulupirira kuti munaturuka kwa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Yohane 16
Onani Yohane 16:30 nkhani