Yohane 17:13 BL92

13 Koma tso pane ndidza kwa Inu; ndipo izi ndilankhula m'dziko lapansi, kuti akhale naco cimwemwe canga cokwaniridwa mwa iwo okha.

Werengani mutu wathunthu Yohane 17

Onani Yohane 17:13 nkhani