Yohane 17:21 BL92

21 kuti onse akakhale amodzi, monga Inu Atate mwa Ine, ndi Ine mwa Inu, kuti iwonso akakhale mwa Ife: kuti dziko lapansi likakhulupire kuti Inu munandituma Ine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 17

Onani Yohane 17:21 nkhani