Yohane 17:23 BL92

23 Ine mwa iwo, ndi Inu mwa Ine, kuti akhale angwiro mwa mmodzi; kutr dziko lapansi lizindikire kuti Inu munandituma Ine, nimunawakonda iwo, monga momwe munakonda Ine,

Werengani mutu wathunthu Yohane 17

Onani Yohane 17:23 nkhani