8 cifukwa mau amene munandipatsa Ine ndinapatsa iwo; ndipo analandira, nazindikira koona kuti ndinaturuka kwa Inu, ndipo anakhulupira kuti Inu munandituma Ine.
Werengani mutu wathunthu Yohane 17
Onani Yohane 17:8 nkhani