2 Koma Yudasenso amene akampereka iye, anadziwa malowa; cifukwa Yesu akamkako kawiri kawiri ndi akuphunzira ace.
Werengani mutu wathunthu Yohane 18
Onani Yohane 18:2 nkhani