Yohane 18:21 BL92

21 Undifunsiranji Ine? funsa iwo amene adamva cimene ndinalankhula nao; taona, amenewo adziwa cimene ndinanena Ine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:21 nkhani