Yohane 18:25 BL92

25 Koma Simoni Petro analikuimirira ndi kuotha moto. Pomwepo anati kwa iye, Suli iwenso wa akuphunzira ace kodi? Iyeyu anakana, nati, Sindine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:25 nkhani