Yohane 18:28 BL92

28 Pamenepo anamtenga Yesu kucokera kwa Kayafa kupita ku Pretorio; koma munali mamawa; ndipo iwo sanalowa ku Pretorio, kuti angadetsedwe, koma kuti akadye Paskha.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:28 nkhani