Yohane 18:31 BL92

31 Ndipo Pilato anati kwa iwo, Mumtenge iye inu, ndi kumweruza iye monga mwa cilamulo canu. Ayuda anati kwa iye, Tiribe ulamuliro wakupha munthu ali yense;

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:31 nkhani