Yohane 18:33 BL92

33 Cifukwa cace Pilato analowanso m'Pretorio, naitana Yesu, nati kwa iye, Iwe ndiwe Mfumu ya Ayuda kodi?

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:33 nkhani