Yohane 18:36 BL92

36 Yesu anayankha, Ufumu wanga suli wa dziko lino lapansi; ufumu wanga ukadakhala wa dziko lino lapansi, anyamata anga akadalimbika nkhondo, kuti ndisaperekedwe kwa Ayuda; koma tsopano ufumu wanga suli wocokera konkuno.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:36 nkhani