Yohane 18:38 BL92

38 Pilato ananena kwa iye, Coonadi nciani? Ndipo pamene adanena ici, anaturukiranso kwa Ayudawo, nanena nao, vine sindipeza konse cifukwa mwa iye.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:38 nkhani