Yohane 20:11 BL92

11 Koma Mariya analikuima kumanda kunja, alikulira. Ndipo m'mene alikulira anawerama cisuzumirire kumanda;

Werengani mutu wathunthu Yohane 20

Onani Yohane 20:11 nkhani