13 Ndipo iwowa ananena kwa iye, Mkazi, uliranji? Ananena nao, Cifukwa anacotsa Ambuye wanga, ndipo sindidziwa kumene anamuika iye.
Werengani mutu wathunthu Yohane 20
Onani Yohane 20:13 nkhani