Yohane 20:17 BL92

17 Yesu ananena naye, Usandikhudze, pakuti sindinatha kukwera kwa Atate; koma pita kwa abale anga, ukati kwa iwo, Ndikwera kunka kwa Atate wanga, ndi Atate wanu, ndi Mulungu wanga, ndi Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 20

Onani Yohane 20:17 nkhani