25 Koma palinso zina zambiri zimene. Yesu anazicita, zoti zikadalembedwa zonse phe, ndilingalira kuti dziko lapansi silikadakhala nao malo a mabuku amene akadalembedwa. Amen.
Werengani mutu wathunthu Yohane 21
Onani Yohane 21:25 nkhani