3 Simoni Petro ananena nao, ndinka kukasodza. Ananena naye, Ifenso tipita nawe. Anaturuka, nalowa m'ngalawa; ndipo m'usiku muja sanagwira kanthu.
Werengani mutu wathunthu Yohane 21
Onani Yohane 21:3 nkhani