Yohane 3:11 BL92

11 Indetu, indetu, ndinena kwa iwe, Tilankhula cimene ticidziwa, ndipo ticita umboni za cimene taeiona; ndipo umboni wathu simuulandira.

Werengani mutu wathunthu Yohane 3

Onani Yohane 3:11 nkhani