Yohane 3:23 BL92

23 Ndipo Yohane analinkubatiza m'Ainoni pafupi pa Salemu, cifukwa panali madzi ambiri pamenepo; ndipo analinkufikako anthu, nalinkubatizidwa.

Werengani mutu wathunthu Yohane 3

Onani Yohane 3:23 nkhani