31 Iye wocokera Kumwamba ali woposa onse; iye amene ali wa dziko lapansi ali wa dziko lapansi, nalankhula za dziko lapansi: Iye wocokera Kumwamba ali woposa onse.
Werengani mutu wathunthu Yohane 3
Onani Yohane 3:31 nkhani