Yohane 3:5 BL92

5 Yesu anayankha, Indetu, indetu, ndinena ndi iwe, Ngati munthu sabadwa mwa madzi ndi Mzimu, sakhoza kulowa ufumu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 3

Onani Yohane 3:5 nkhani