8 Mphepo iomba pomwe ifuna, ndipo ukumva mau ace, komavsudziwa, kumene icokera, ndi kumene imuka; cotero ali yense wobadwa mwa Mzimu.
Werengani mutu wathunthu Yohane 3
Onani Yohane 3:8 nkhani