25 Mkazi ananena ndi Iye, Ndidziwa kuti Mesiya adza (wochedwa Kristu): akadzadza Iyeyu, adzatiuza zonse.
Werengani mutu wathunthu Yohane 4
Onani Yohane 4:25 nkhani