Yohane 4:27 BL92

27 Ndipo pamenepo anadza ophunzira ace; nazizwa kuti analinkulankhula ndi mkazi; koma panalibe wina anati, Mufuna ciani? kapena, mulankhula naye ciani?

Werengani mutu wathunthu Yohane 4

Onani Yohane 4:27 nkhani