25 Indetu, indetu, ndinena kwa inu, kuti ikudza nthawi, ndipo Iripo tsopano, imene akufa adzamva mau a Mulungu; ndipo iwo akumva adzakhala ndi moyo.
Werengani mutu wathunthu Yohane 5
Onani Yohane 5:25 nkhani