44 Mungathe inu bwanji kukhulupira, 5 popeza mulandira ulemu wina kwa mnzace ndipo ulemu wakucokera kwa Mulungu yekha simuufuna?
Werengani mutu wathunthu Yohane 5
Onani Yohane 5:44 nkhani