Yohane 6:17 BL92

17 ndipo pamene adalowa m'ngalawa, analikuoloka nyanja kunka ku Kapernao. Ndipo kutada pamenepo, koma Yesu asanadze kwa iwo.

Werengani mutu wathunthu Yohane 6

Onani Yohane 6:17 nkhani