Yohane 6:24 BL92

24 cifukwa cace pamene khamu la anthu linaona kuti palibe Yesu, ndi akuphunzira ace palibe, iwo okha analowa m'ngalawazo nadza ku Kapernao, alikufuna Yesu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 6

Onani Yohane 6:24 nkhani