Yohane 6:41 BL92

41 Cifukwa cace Ayuda anang'ung'udza za iye, cifukwa anati, Ine ndine mkate wotsika Kumwamba.

Werengani mutu wathunthu Yohane 6

Onani Yohane 6:41 nkhani