Yohane 6:5 BL92

5 Pamenepo Yesu, pokweza maso ace, ndi kuona kuti khamu lalikuru lirinkudza kwa iye, ananena kwa Filipo, Tidzagula kuti mikate kuti adye awa?

Werengani mutu wathunthu Yohane 6

Onani Yohane 6:5 nkhani