Yohane 7:17 BL92

17 Ngati munthu ali yense afuna kucita cifuniro cace, adzazindikira za ciphunzitsoco, ngati cicokera kwa Mulungu, kapena ndilankhula zocokera kwa Ine ndekha.

Werengani mutu wathunthu Yohane 7

Onani Yohane 7:17 nkhani