Yohane 7:39 BL92

39 Koma 1 ici anati za Mzimu, amene iwo akukhulupirira iye anati adzalandire; pakuti Mzimu panalibe pamenepo, cifukwa Yesu sanalemekezedwa panthawi pomwepo.

Werengani mutu wathunthu Yohane 7

Onani Yohane 7:39 nkhani