Yohane 7:7 BL92

7 Dziko lapansi silingathe kudana ndi inu; koma Ine lindida popeza Ine ndilicitira umboni, kuti nchito zace ziri zoipa,

Werengani mutu wathunthu Yohane 7

Onani Yohane 7:7 nkhani