12 Pamenepo Yesu analankhulanso nao, nanena, Ine ndine kuunika kwa dziko lapansi; iye wonditsata ine sadzayenda mumdima, koma adzakhala nako kuunika kwa moyo.
Werengani mutu wathunthu Yohane 8
Onani Yohane 8:12 nkhani