Yohane 8:26 BL92

26 Ndiri nazo zambiri zakulankhula ndi zakuweruza za inu; koma wondituma Ine ali woona; ndipo zimene ndazimva kwa iye, zomwezo ndilankhuia kwa dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yohane 8

Onani Yohane 8:26 nkhani