Yohane 8:39 BL92

39 Anayankha nati kwa iye, Atate wathu ndiye Abrahamu. Yesu ananena nao, 2 Ngati muli ana a Abrahamu, mukadacita nchito za Abrahamu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 8

Onani Yohane 8:39 nkhani