Yohane 8:52 BL92

52 Ayuda anati kwa Iye, Tsopano tazindikira kuti muli ndi ciwanda. 10 Abrahamu anamwalira, ndi aneneri; ndipo Inu munena, Munthu akasunga mau anga, sadzalawa imfa ku nthawi yonse.

Werengani mutu wathunthu Yohane 8

Onani Yohane 8:52 nkhani