Yohane 8:54 BL92

54 Yesu anayankha, Ngati Ine ndidzilemekeza ndekha, ulemerero wanga uli cabe; 11 Atate wanga ndiye wondilemekeza Ine; amene munena za iye, kuti ndiye Mulungu wanu;

Werengani mutu wathunthu Yohane 8

Onani Yohane 8:54 nkhani