Yohane 9:21 BL92

21 koma sitidziwa umo apenyera tsopano; kapena sitimdziwa amene anamtsegulira pamaso pace; mumfunse iye; ali wamsinkhu; adzalankhula mwini za iye yekha.

Werengani mutu wathunthu Yohane 9

Onani Yohane 9:21 nkhani