Yohane 9:39 BL92

39 Ndipo Yesu anati, Kudzaweruza ndadza Ine ku dziko lino lapansi, kuti iwo osapenya apenye; ndi kuti iwo akupenya akhale osaona,

Werengani mutu wathunthu Yohane 9

Onani Yohane 9:39 nkhani