2 Samueli 22:8 BL92

8 Pomwepo dziko linagwedezeka ndi kunthunthumira.Maziko a dziko la kumwamba anasunthikaNagwedezeka, cifukwa iye anakwiya.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 22

Onani 2 Samueli 22:8 nkhani