1 Ndipo m'tsogolo mwace Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa; Davide nalanda mudzi wa Metege Ama m'manja mwa Afilisti.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8
Onani 2 Samueli 8:1 nkhani