2 Samueli 8:2 BL92

2 Ndipo anakantha Amoabu nawayesa ndi cingwe, nawagonetsa pansi; ndipo anawayesera zingwe ziwiri kupha, ndi cingwe cimodzi cathunthu kusunga ndi moyo. Ndipo Amoabu anakhala anthu a Davide, nabwera: nayo mitulo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8

Onani 2 Samueli 8:2 nkhani