2 Samueli 8:3 BL92

3 Davide anakanthanso Hadadezeri, mwana wa Rehobu, mfumu ya ku Zoba, pomuka iye kukadzitengeranso ufumu wace ku cimtsinje ca Firate.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 8

Onani 2 Samueli 8:3 nkhani