26 Ndipo munthuyo anamuka ku dziko la Ahiti, namanga mudzi, naucha dzina lace Luzi; ndilo dzina lace mpaka lero lino.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 1
Onani Oweruza 1:26 nkhani