Oweruza 1:35 BL92

35 Aamori anakhumbanso kukhala ku phiri la Heresi, ku Ajaloni, ndi ku Saalibimu; koma dzanja la a m'nyumba ya Yosefe linawalaka, nakhala iwo akupereka msonkho.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 1

Onani Oweruza 1:35 nkhani